Abale ndi Alongo,
Chaka chisanathe ichi ndati nane ndikufunileni nonse mafuno abwino a khirisimisi ndi nyuwele.Nthawi imeneyi kwathu ku Chitakale imakhala nthawi yokoma kwambiri chifukwa anthu amachalira kutchena ndi kudya zanoninoni,inu mupanganji kodi?
Mele Khirisimasi and Hape nyuwele!!
ifetu tingolota zakushift kufuna kulandira zambiri. kwa anzathunu tikuti sangalalani bwino koma avoid drinking and driving chifukwa moyo udakakoma.