Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: tchekela ma pounds


Newbie

Status: Offline
Posts: 23
Date:
tchekela ma pounds
Permalink Closed


Villagers no longer walk few hours to fetch water since the Malawi Red Cross built a water pump for the community in the village of Ngonodnda, Dedza district, Malawi.


 


ndayenda  kutauni  ntchito


ndayenda   kuntandile 


ndatchekela maluzi


aa  ine ine ndangosanduka  olira


ndatchekela maluzi


ine ine


ndinali munthu kale  ndikagula mowa ngati madeya


ndinali ndi anzanga tigula mowa  aknimwera sindikadela  nkhawa koma lero ali kuti


umaziwa ku diabora  heinkein tiye tiye   uyoooooooo


wayiwala  kumudzi ndi bekhi  ayi ayi


ndatchekela mluzi ndalephera ine 



__________________


Newbie

Status: Offline
Posts: 1
Date:
RE: tchekela ma Euro
Permalink Closed


Ndayendayenda mu Blantyre ntchito osayipeza.


Digiri inkangofumbwa...mabwana akuvuna ekesipiriyensi...


Bwana ''Inu ochuluka nzeru ayi - tikufuna a hands-on...' ...Poly Poly ndiye kuti chiyani''


Mtsuko'' Tikangopangapo sukulu apa'' 


Tchekela ma euro...


 


 



__________________


Guru

Status: Offline
Posts: 2423
Date:
RE: tchekela ma pounds
Permalink Closed


A very beautiful picture indeed... Where did you get it from?

__________________


Guru

Status: Offline
Posts: 1215
Date:
Permalink Closed

 


mkazi wonunkha chifwenthe ndi thukuta,oh how i miss the motherland!!!



__________________
all i have is my word,and i dont break it for nobody.


Guru

Status: Offline
Posts: 1277
Date:
Permalink Closed

game wrote:


  mkazi wonunkha chifwenthe ndi thukuta,oh how i miss the motherland!!!

Lol!! and her kiss( a dry one)

__________________
If Iam not for myself,who will be for me?And if Iam only for myself,what am I?


Senior Member

Status: Offline
Posts: 169
Date:
Permalink Closed

Mkanziyu zake zonse ndiza lokolo Kuyambira



  1. Fungo
  2. Thukuta
  3. Panti mwinanso alibe
  4. Akatumba opopa
  5. Zikakhala zinazo ndiye she can provide a very good macina de concreto and Zimbabwe Airways under instructions from her Namkungwi or Ngaliba
  6. She likes it in total darkness and what you should do is to pretend as if you have J.Lo or Beyonce or Shakira then you will have a good one.
  7. Koma kulikonse uzipita you will have her Thukuta Smell and Other smells which I cannot be described but anyway that is what you expect from a local breed

I miss the smell WHICH SHE CAN PROVIDE AFTER HUGGING HER



__________________


Newbie

Status: Offline
Posts: 23
Date:
Permalink Closed

chipwilikiti    paliponse  asokoneza 


 


chiphwikiliti   mwina mfanzi sikumva  we talk about creation and pollution  panopa zafika povuta  mababe  awa ndi abwino  koma  akabwera  kuno kunja  eeeeeee mixed  vegs


kunyasa  akavala  mini  scooter ndi mabele things fallen apart  why why why ma member moti


pap smear imavuta fungo  lamix  perfumes ndi natural odour


kudabwa  mtala  mweni ayipisa


mimba mukuwawa  ndi pambuke pompa


wathapu wathapu man



__________________


Newbie

Status: Offline
Posts: 2
Date:
Permalink Closed

wachifwenthe ali bwino kwabasi  ndidayenda mwinanu koma ayi kafungo kaja kali bwino maka kamumdimako ndiye amachita kukuwa

__________________
angonikukwata


Veteran Member

Status: Offline
Posts: 140
Date:
Permalink Closed

Musakhale ngati simukhalepo kapena kugona ndi akazi oterewo. Yimakhala original bambo, zantchito kawawa.

__________________
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard