Iam quite concerned with the way Malawian ladies are behaving in this country. Kaya ndikusowa mapepala koma mwaonjeza. Kazipitani kumudzi mungotolanazo azungu osasamba kaye Manchester. What are your views about this anthuni???????
Mmesa ine ndinamva kuti ku manchester amuna ake amangokhala chiledzelele and ndi aja okuti ku Malawi amakhala ku boys quarters ndiye mmadziwa zoziwonela kuu...... Thats why upeza akazi apamalawi akuyenda ndi azungu or amuna amayiko ena or amalawi ama city ena. To be honest amuna enieni tinawasiya ku malawi, osamanga zingongo,ovala ma suit monday to friday week end kukutenga ku lake, ma manager ama company. osati za zii za munozi. no offence. Shaaaaaaa.
Ha ha Mmesa ine ndinamva kuti ku manchester amuna ake amangokhala chiledzelele and ndi aja okuti ku Malawi amakhala ku boys quarters ndiye mmadziwa zoziwonela kuu...... Thats why upeza akazi apamalawi akuyenda ndi azungu or amuna amayiko ena or amalawi ama city ena. To be honest amuna enieni tinawasiya ku malawi, osamanga zingongo,ovala ma suit monday to friday week end kukutenga ku lake, ma manager ama company. osati za zii za munozi. no offence. Shaaaaaaa.-- Edited by Thabwa at 17:31, 2006-02-01
Thats true gal, tikafuna amuna achiMalawi tikawapeza ku mudzi konko. Is it cos u r from Malawi u should go out with ur fellow Malawians
Mumadziwana eti? Amalawi kondanani. Ku america amalawitu akukwatitsa. Anthu mumamwera mowa pamodzi koma chikondi sichikufikabe shaa!! Reminds me of a chap I used to know back in LL who seems desperate to have a white girlfriend and every month we meet, he seems to be getting better at choosing, in terms of torso size. Zochezatu izi. Kugunda mtengo mchamuna chomwe!!
we go abroad with different minds,views and whatever ........amriri amapita kuti ndi kaone mzungu ali bwanji kusiyanitsa akuti,kuyendera ija yoti "kudya nkudya bola kuasala mwala"
Sibwino kunyozana amalawi. Makondamakonda mwina ena afuna osasambawo. Even azungu sasamba and we are better than them. Ifenso tinali choncho nthawi ina koma pano ndife anthu olozeka. Zonse ndi nthawi basi.