MUPANGA BWANJI POVERTEY HISTORY NDI MOWA AND VINTHULI VA NYAMA YA GWAPE ? YOU ARE NOT VERY MUCH SERIOUS ETI. SO YOU HAVE BEERS FROM MALAWI . HEHEDE!!!BWANJI OSAWONJEZERA KA KADAMSANA KOTHYAKULA BWINO KAMAKONO.
MUZIUZANA ZAKUPSA KUMENEKO OSATI NDEU KAPENA KUKAMBILANA ZOTI INE VETERAN MEMBER PANO MUNDICHOTSE.NONSE MUTHA INE NDILIPO. KUNGOTI NTHAWI ZINA MAGESI AMAVUTAVUTA CHABE KOMA NKHOTO ILIPO CHIFUKWA MUNAYAMBA ZIBWANA NOKHA ZOFUNA KUNDICHOTSA.
KUNONSO PATE ILPO SABATA YAMAWA KU AREA 47 SECTAR 5 HOUSE NUMBER 456. NOT ALL INVITED . SIZABOMA IZI KOMA ZANTCHITO.