Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: USELESS AND SENSILESS REPLIES


Senior Member

Status: Offline
Posts: 151
Date:
USELESS AND SENSILESS REPLIES
Permalink Closed


Thank you: Mr Petre Griffin . Iwe nde mzanazanga ndithu. Umakamba za nzeru ngati bambo uyu nwayambitsa izi , Eetchef , inde ngosokoneza ndithu .


I dont hav respect for these useless members who have wanted always commenting and responding to everybody here . Who are these people, these are poisons here because they reply with nonsense but kufuna kudziwonetsera kuti amabwereka komputer. Dzulo titawerenga zolemba zambiliko ndithu pano tapedzapo kuti pali anthu ena muno mumabwebweta kwambili, kodi vuto lanu niliti kodi. Kukamwa tsegu ngati gulugufe nthawi zonse. Kodi Malawiana ndi ankulo wanu kapena chiwongo cahazakhali wanu. Chete alifunika pano nthawi zina. Pali ena amafikitsa topics yokomera ndithu ndithu koma chifukwa walemba mchizungu chamkalasi osati chapamowa kapena pa kantini mumamfikila kukamwa yasa . AHH! Nyasi pano ayi , Uve yayi .


Please weni ake bwalo lino wauzeni wonse awa : Mzimayi wachimasomaso uyu Chiki, Chichi, Anyakwawa Game, Sepulani, Bambo wa dama Moneylow, Mbusa Davie,Che  Abiti Nyono, Bambo Kesso, Malemu Geuvara, Nyapala Blackpanther, nthumbidwa wapa resthouse ku Lunzu Sexmadsista ndi wena kuti Apeze chochita china . Mungamanene kuti ndimadrinka Kadansana ine : Haa I drunk Specialo, Ine NJINGA : MAINE, i Have a car from Darbun , INU MULI NDI CHANI? Bulukhu la ine you think zamasewera eti, inu simuval mabotolo achi yoo ndi rastaman.


Werengani momvetsa chiyankhulo matopi wonga a Ayatollah, Chegyavara, Eetchef , Davidia, Js, and uyu PeterGriffin.....Sukulu imawoneka ndithu osati milomo yaviyavi.



-- Edited by NYASALAND at 15:57, 2005-06-01

__________________
Zikomo


Newbie

Status: Offline
Posts: 20
Date:
Permalink Closed

KODI AWANSO NDE ATI ?? ACHOKELA KUTI ???

DUDE ARE YOU A MAN OR A WOMAN , COS NGATI ULIMAMUNA NDE NDIWE OLALATATU

CHILETSO NDITHU

AMENE AKUKUKAKAMIZA KUTI UZIWELENGA MA TOPIKI PANO NDINDANI??

O DI APA NDIZIPITA INE , MUYAMBA KUNDI YAKHULITSA PAMBALI

IFETU PANO NDI PANCHENGA




__________________
Warona


Senior Member

Status: Offline
Posts: 151
Date:
Permalink Closed

Masipeko wrote:


KODI AWANSO NDE ATI ?? ACHOKELA KUTI ??? DUDE ARE YOU A MAN OR A WOMAN , COS NGATI ULIMAMUNA NDE NDIWE OLALATATU CHILETSO NDITHU AMENE AKUKUKAKAMIZA KUTI UZIWELENGA MA TOPIKI PANO NDINDANI?? O DI APA NDIZIPITA INE , MUYAMBA KUNDI YAKHULITSA PAMBALI IFETU PANO NDI PANCHENGA

Iweyo ndi munthu wodwala eti. Iwe wulindifusa za ine nanga iwe ndi yani? Iwe ndiye Nguli ija amanena Bambo Kesso ija, nguli yothawila kunsi kwa bafa ku Magwero. Apa pakhalanso panchenga bwanji , nanga mukathilana mchenga mkhutu. Kodi iwe ukunyoza azimayi kuti ngolongolola eti . Khala chete ndikubweza kumena uliko, I can bought yu a ticket plus kamba mnjila. Fotseki

__________________
Zikomo


Newbie

Status: Offline
Posts: 20
Date:
Permalink Closed

Iweyo ndi munthu wodwala eti. Iwe wulindifusa za ine nanga iwe ndi yani? Iwe ndiye Nguli ija amanena Bambo Kesso ija, nguli yothawila kunsi kwa bafa ku Magwero. Apa pakhalanso panchenga bwanji , nanga mukathilana mchenga mkhutu. Kodi iwe ukunyoza azimayi kuti ngolongolola eti . Khala chete ndikubweza kumena uliko, I can bought yu a ticket plus kamba mnjila. Fotseki


AMATI VOETSEK MWANVA GOMANI !!!!!!


KUKONDA ZINTHU BWANJI  BAMBO 


TABAKWELANI NJINGA YANUYO PAMENEPO  , MUGWATU


INUYO MWANGOSOWA ZOKAMBA YAPA  , TNAKANI UKO , MUSATITOPETSE IFE PANO  , IFE BASI NJENJENJE KUTI PABWERA A NYASALANDI PANO 


ALA! NDE ZOKANIKAZO ZIMENEZO


 




 



__________________
Warona


Senior Member

Status: Offline
Posts: 423
Date:
Permalink Closed

Personally, Im voting Nyasaland off this forum. from now on i will not respond to any of his messages until he talks some sense. I feel like i am wasting precious time by writing this reponse to him. He is probably some guy just trying to get kicks off people - no time for that - Im out.

__________________


Member

Status: Offline
Posts: 71
Date:
Permalink Closed

NYASALAND wrote:


Thank you: Mr Petre Griffin . Iwe nde mzanazanga ndithu. Umakamba za nzeru ngati bambo uyu nwayambitsa izi , Eetchef , inde ngosokoneza ndithu . I dont hav respect for these useless members who have wanted always commenting and responding to everybody here . Who are these people, these are poisons here because they reply with nonsense but kufuna kudziwonetsera kuti amabwereka komputer. Dzulo titawerenga zolemba zambiliko ndithu pano tapedzapo kuti pali anthu ena muno mumabwebweta kwambili, kodi vuto lanu niliti kodi. Kukamwa tsegu ngati gulugufe nthawi zonse. Kodi Malawiana ndi ankulo wanu kapena chiwongo cahazakhali wanu. Chete alifunika pano nthawi zina. Pali ena amafikitsa topics yokomera ndithu ndithu koma chifukwa walemba mchizungu chamkalasi osati chapamowa kapena pa kantini mumamfikila kukamwa yasa . AHH! Nyasi pano ayi , Uve yayi . Please weni ake bwalo lino wauzeni wonse awa : Mzimayi wachimasomaso uyu Chiki, Chichi, Anyakwawa Game, Sepulani, Bambo wa dama Moneylow, Mbusa Davie,Che  Abiti Nyono, Bambo Kesso, Malemu Geuvara, Nyapala Blackpanther, nthumbidwa wapa resthouse ku Lunzu Sexmadsista ndi wena kuti Apeze chochita china . Mungamanene kuti ndimadrinka Kadansana ine : Haa I drunk Specialo, Ine NJINGA : MAINE, i Have a car from Darbun , INU MULI NDI CHANI? Bulukhu la ine you think zamasewera eti, inu simuval mabotolo achi yoo ndi rastaman. Werengani momvetsa chiyankhulo matopi wonga a Ayatollah, Chegyavara, Eetchef , Davidia, Js, and uyu PeterGriffin.....Sukulu imawoneka ndithu osati milomo yaviyavi. -- Edited by NYASALAND at 15:57, 2005-06-01

Mr Nyasaland you really know how to stir **** up,causing confusion, disturbing the peace,I think you are great but chill out abit, stop attacking please, I like you on this forum but sometimes you get tooooooo personal. Why are you so aggressive?Do you hate everyone or are you just trying to be a bad boy??try to be sociable please because at the moment you are not and i know that you are going to reply with alot of insults but hey!!Will I be surprised??Don't be so predictable ok?

__________________
........So help me God


Senior Member

Status: Offline
Posts: 423
Date:
Permalink Closed

I think its a classic case of the Drama Queen

__________________


Senior Member

Status: Offline
Posts: 397
Date:
Permalink Closed

This Nyasaland Guy is really a pain in the ass , he is a like a blood sucking tick you know!


DUDE IF YOU AINT GOT ANYTHING TO SAY ON THIS FORUM  , IT BEST YOU BOUNCE


COS YOU REALLY PISSING ME OFF 


Am with panther guys  , this dude got to go  , looks like he's looking for trouble 


dont give the pleasure 


*kiss*


 



__________________
SUN GODDE'SS (The Earth Mother , Queen of Africa and Warrior Activist and Conqueror Ancestral Spirit and Revolutionary Mayibuye!)


Newbie

Status: Offline
Posts: 23
Date:
Permalink Closed

Sonny boi,


you sure can write crap!GO BACK TO WHERE YOU BELONG!Let the men do mens work,and you,you damn well know where!STANDARD 8c CLASS.


P.S.good luck with your exams!



__________________


Veteran Member

Status: Offline
Posts: 120
Date:
Permalink Closed

I think much time has been spent on this dude arleady.  Not worth it at all. PRICK!!!



__________________
Trials. Use them to ur advantage. Come out stronger on the other side!


Newbie

Status: Offline
Posts: 31
Date:
Permalink Closed

If you argue with a fool,noone wil notice the difference btwn you & the fool.


Forget the dude and lets concentrate on real issues.



__________________
When I read the Evils of Alcohol,I gave up reading!


Senior Member

Status: Offline
Posts: 240
Date:
Permalink Closed

Hey ya'll if pple ignore this guy he will have nothing to say.  He is just looking for attention and ya'll are giving it to him.  His posting doesnt even make sense so why waste time on him


I think there better things to discuss



__________________
Jesus is the answer for the world today and above him there is no other
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard