Thank you: Mr Petre Griffin . Iwe nde mzanazanga ndithu. Umakamba za nzeru ngati bambo uyu nwayambitsa izi , Eetchef , inde ngosokoneza ndithu .
I dont hav respect for these useless members who have wanted always commenting and responding to everybody here . Who are these people, these are poisons here because they reply with nonsense but kufuna kudziwonetsera kuti amabwereka komputer. Dzulo titawerenga zolemba zambiliko ndithu pano tapedzapo kuti pali anthu ena muno mumabwebweta kwambili, kodi vuto lanu niliti kodi. Kukamwa tsegu ngati gulugufe nthawi zonse. Kodi Malawiana ndi ankulo wanu kapena chiwongo cahazakhali wanu. Chete alifunika pano nthawi zina. Pali ena amafikitsa topics yokomera ndithu ndithu koma chifukwa walemba mchizungu chamkalasi osati chapamowa kapena pa kantini mumamfikila kukamwa yasa . AHH! Nyasi pano ayi , Uve yayi .
Please weni ake bwalo lino wauzeni wonse awa : Mzimayi wachimasomaso uyu Chiki, Chichi, Anyakwawa Game, Sepulani, Bambo wa dama Moneylow, Mbusa Davie,Che Abiti Nyono, Bambo Kesso, Malemu Geuvara, Nyapala Blackpanther, nthumbidwa wapa resthouse ku Lunzu Sexmadsista ndi wena kuti Apeze chochita china . Mungamanene kuti ndimadrinka Kadansana ine : Haa I drunk Specialo, Ine NJINGA : MAINE, i Have a car from Darbun , INU MULI NDI CHANI? Bulukhu la ine you think zamasewera eti, inu simuval mabotolo achi yoo ndi rastaman.
Werengani momvetsa chiyankhulo matopi wonga a Ayatollah, Chegyavara, Eetchef , Davidia, Js, and uyu PeterGriffin.....Sukulu imawoneka ndithu osati milomo yaviyavi.
KODI AWANSO NDE ATI ?? ACHOKELA KUTI ??? DUDE ARE YOU A MAN OR A WOMAN , COS NGATI ULIMAMUNA NDE NDIWE OLALATATU CHILETSO NDITHU AMENE AKUKUKAKAMIZA KUTI UZIWELENGA MA TOPIKI PANO NDINDANI?? O DI APA NDIZIPITA INE , MUYAMBA KUNDI YAKHULITSA PAMBALI IFETU PANO NDI PANCHENGA
Iweyo ndi munthu wodwala eti. Iwe wulindifusa za ine nanga iwe ndi yani? Iwe ndiye Nguli ija amanena Bambo Kesso ija, nguli yothawila kunsi kwa bafa ku Magwero. Apa pakhalanso panchenga bwanji , nanga mukathilana mchenga mkhutu. Kodi iwe ukunyoza azimayi kuti ngolongolola eti . Khala chete ndikubweza kumena uliko, I can bought yu a ticket plus kamba mnjila. Fotseki
Iweyo ndi munthu wodwala eti. Iwe wulindifusa za ine nanga iwe ndi yani? Iwe ndiye Nguli ija amanena Bambo Kesso ija, nguli yothawila kunsi kwa bafa ku Magwero. Apa pakhalanso panchenga bwanji , nanga mukathilana mchenga mkhutu. Kodi iwe ukunyoza azimayi kuti ngolongolola eti . Khala chete ndikubweza kumena uliko, I can bought yu a ticket plus kamba mnjila. Fotseki
AMATI VOETSEK MWANVA GOMANI !!!!!!
KUKONDA ZINTHU BWANJI BAMBO
TABAKWELANI NJINGA YANUYO PAMENEPO , MUGWATU
INUYO MWANGOSOWA ZOKAMBA YAPA , TNAKANI UKO , MUSATITOPETSE IFE PANO , IFE BASI NJENJENJE KUTI PABWERA A NYASALANDI PANO
Personally, Im voting Nyasaland off this forum. from now on i will not respond to any of his messages until he talks some sense. I feel like i am wasting precious time by writing this reponse to him. He is probably some guy just trying to get kicks off people - no time for that - Im out.
Thank you: Mr Petre Griffin . Iwe nde mzanazanga ndithu. Umakamba za nzeru ngati bambo uyu nwayambitsa izi , Eetchef , inde ngosokoneza ndithu . I dont hav respect for these useless members who have wanted always commenting and responding to everybody here . Who are these people, these are poisons here because they reply with nonsense but kufuna kudziwonetsera kuti amabwereka komputer. Dzulo titawerenga zolemba zambiliko ndithu pano tapedzapo kuti pali anthu ena muno mumabwebweta kwambili, kodi vuto lanu niliti kodi. Kukamwa tsegu ngati gulugufe nthawi zonse. Kodi Malawiana ndi ankulo wanu kapena chiwongo cahazakhali wanu. Chete alifunika pano nthawi zina. Pali ena amafikitsa topics yokomera ndithu ndithu koma chifukwa walemba mchizungu chamkalasi osati chapamowa kapena pa kantini mumamfikila kukamwa yasa . AHH! Nyasi pano ayi , Uve yayi . Please weni ake bwalo lino wauzeni wonse awa : Mzimayi wachimasomaso uyu Chiki, Chichi, Anyakwawa Game, Sepulani, Bambo wa dama Moneylow, Mbusa Davie,Che Abiti Nyono, Bambo Kesso, Malemu Geuvara, Nyapala Blackpanther, nthumbidwa wapa resthouse ku Lunzu Sexmadsista ndi wena kuti Apeze chochita china . Mungamanene kuti ndimadrinka Kadansana ine : Haa I drunk Specialo, Ine NJINGA : MAINE, i Have a car from Darbun , INU MULI NDI CHANI? Bulukhu la ine you think zamasewera eti, inu simuval mabotolo achi yoo ndi rastaman. Werengani momvetsa chiyankhulo matopi wonga a Ayatollah, Chegyavara, Eetchef , Davidia, Js, and uyu PeterGriffin.....Sukulu imawoneka ndithu osati milomo yaviyavi. -- Edited by NYASALAND at 15:57, 2005-06-01
Mr Nyasaland you really know how to stir **** up,causing confusion, disturbing the peace,I think you are great but chill out abit, stop attacking please, I like you on this forum but sometimes you get tooooooo personal. Why are you so aggressive?Do you hate everyone or are you just trying to be a bad boy??try to be sociable please because at the moment you are not and i know that you are going to reply with alot of insults but hey!!Will I be surprised??Don't be so predictable ok?
Hey ya'll if pple ignore this guy he will have nothing to say. He is just looking for attention and ya'll are giving it to him. His posting doesnt even make sense so why waste time on him
I think there better things to discuss
__________________
Jesus is the answer for the world today and above him there is no other