Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: ladies must be serious


Newbie

Status: Offline
Posts: 1
Date:
ladies must be serious
Permalink Closed


I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja. 

__________________
i sign


Guru

Status: Offline
Posts: 651
Date:
Permalink Closed

quote:

Originally posted by: masikini

"I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja. "

ikuyambila pati kodi nkhaniyi?wasiyidwayo ndani?

__________________
For have I now become your enemy for telling you the truth?-Galatians 4 v16.


Veteran Member

Status: Offline
Posts: 120
Date:
Permalink Closed

quote:

Originally posted by: masikini

"I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja. "


Amwene


Pofunikatu kufotokoza bwinobwino pamenepa.



__________________
Trials. Use them to ur advantage. Come out stronger on the other side!


Member

Status: Offline
Posts: 71
Date:
Permalink Closed

Why should it always be up to the woman to keep the marriage together?IT TAKES TWO TO TANGO

__________________
........So help me God
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard