I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja.
quote: Originally posted by: masikini "I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja. "
ikuyambila pati kodi nkhaniyi?wasiyidwayo ndani?
__________________
For have I now become your enemy for telling you the truth?-Galatians 4 v16.
quote: Originally posted by: masikini "I must introduce or rather remind my dear countrymen kuti atsikana athuwa akamabwera kucho kera kumudzi adzilangidwako ndi azimayi akuluakulu pa zakhalidwe la mu banja. It is pitiful to see families breaking apart and hearing kuti mkazi wachoka mu nyumba ya mwamuna wake chifukwa choti ayambana. Tiyeni tilemekeze chikhalidwe chathu. Remember that every problem has a solution. osati kuchoka mu nyumba. Amunanso tisiye kugwiragwira. Kuzembera mkazi. Tiyeni tilemekeze mabanja. "
Amwene
Pofunikatu kufotokoza bwinobwino pamenepa.
__________________
Trials. Use them to ur advantage. Come out stronger on the other side!