Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: ziphuphu za chopper
gibson kalindawalo

Date:
ziphuphu za chopper
Permalink Closed


guys anthu muna tenga ma photo ndi chopper nu aaaH mwandikhumudwisa amalawi ziphuphu zonse zija basi mwati mujambulise ndi macelebrity osasambawo bola sarah koma chopper nde ayi... ziphuphu ngati anamutemera

__________________
linda

Date:
Permalink Closed

kodi a gibowo akuchokera kuti sopano, nyamata miseche ngati mkazi

__________________
fresh

Date:
Permalink Closed

kodi nsanje bwanji a gibo anzanu asanjo pa america inu tionesteni anthu opana ziphuphuwo


 



__________________
Observer

Date:
Permalink Closed

Gibo is just trying to say that Chopper needs some space kuti aphulitse ziphuphu. He needs Ambi shubaba from Malawi. I wouldnt want to be in the same room with him when he detonates those ziphuphu. Watch out, incoming...!

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


ichi ndiye chibwana ichi...


first things first..a gifiti, siyani mabodza meni! kungokhala ngati nankhoviwa bwanji munthu wamamuna..


secondly, inu amane mukumubakira gibo kunyoza ziphuphu za anzanu ndichamba chimenecho, inuyo kuti chani? kusamba? aliyense ali ndi vuto lina lake pathupi pake and leave munthu amene ali ndi zihuphu alone.


ndkati ndiyambe kunena za mavuto a enanu ndiye worse, winawe ukadzuka you soend at least 20 minutes trying to di-entangle ubweya wokolana ndi zofunda, kungokhala ndi matupi a ubweya ngati chiyenda yekha!!


leave the bro alone ........he didn't choose to be like that........



__________________
Observer

Date:
Permalink Closed

This ziphuphu issue seem to be rubbing pple the wrong way. Wonder what that means? Could it be..........lol.....that tapweteka achibale. he he he

__________________
Zina kumanena

Date:
Permalink Closed

Zoti chopper ndi american amadziwa yekha. The first time I saw the brotha I thought he was from beira, Mozambique.

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


magaye munthu anakulakwirani chani?


musiyeni nzanu atase monga mutasila inu........



__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

ise zinakumanena iwe nde nyatwa zoona inenso ndi mayesa kuti chooper ndi waku mozambique kunyasa ngati analakwa pobadwa bwanji iii zosekesa kwabasi

__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

ise observer i think ndapweteka  achibale chifukwa ena zaakhuza kwa basi

__________________
Observer

Date:
Permalink Closed

Gibo, even our boys back at Bwandilo would agree that ziphuphu za chopper ndi zima jawbreaker.



__________________
Iyayi

Date:
Permalink Closed

Ziphuphu zimenezija akuwoneka ngati wavala costume ya halloween. Nanunso atsikana kumangothyokela khosi zilizonse. You will be spending your days detonating chopper's ziphuphu.

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


aaahhh!!


i wont comment anymore on this issue, all i have seen is you two guys are HATERS. hating cuz your friend is able to get hoochies. now that explains it.



__________________
Observer

Date:
Permalink Closed

Which hoochies are you talking about controversy? And he/you calls that an achievement? Zina ukaona my brotha, kamba anga mwala oyi!

__________________
dema

Date:
Permalink Closed

iwe control......... nadkuziwatu ine HE/SHE pusi waipa chani tsopano mesa umabwera ndi fire tiye nazo

__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

ise observer takatengesa ka control>>>> ndiye kaopa sopano thanks to dema HE/SHE ameneyu asatitopese

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


 a fella,


sindimagonja zachamba ine mwamva...too wicked to give in just like that...


bust because i backed off you think am a coward?


mukulenga nonse,


kuli anjiba kuno!!!!!!!!!!!



__________________
Observer

Date:
Permalink Closed

Contro, Ludzu bwa? relax and have a glass of water.

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


ada gibo..


nkhani zathu zisaolokere kwamakolo..lets just deal with it right here...


and oh!! ine ndilibe ziphuphu meni!! kamwana kakamuna kosalala ngati matako amwana wobadwa dzulo....and am cute ....the difference is i know you are ugly....lol



__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

choka iwe auze masteni akugulire ambi shubaba ulinazo ngati ma jawbreaker mwinanso bola za chooper ndakuziwa sopano


 



__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


anamwali inunso kujeda!!


mpaka kumwela madzi...amuna a ntundu wanji? mwina you guys are gays isn't it?



__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

control u kuona ngati tagonja uziwanso mphwanga tiye nazo

__________________
observer

Date:
Permalink Closed

talk to you guys later. Gotta go

__________________
controversial

Date:
Permalink Closed

 


mnzako wathawatu...iwe ndiye ukuti chani?


 



__________________
gibo

Date:
Permalink Closed

nanga zikukhalangati zikukupweteka bwanji za ziphuphuzo kapena madam anakupasani zozolazola kuti musalale ngati matako a mwanawo i think madam anu anpirila kwa basi pano ndemukuti munasalala eti chifukwa mene ndinakuona muja unali nazo zedi zimajawbraker zeni zeni



__________________
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard