Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: MAKALATA AND TS YAKE


Newbie

Status: Offline
Posts: 28
Date:
MAKALATA AND TS YAKE
Permalink Closed


It is with disapointment that the Man i voted for has lost the Elections.I hope other Malawians/Americans i.e mbilkunjanji and others i dont know share the concern,that is if they voted for Kerry.


Chifukwa chodandaulira ndichakuti.....................enanu simuli ku Amelekako ngati oti muli ku sukulu,kapena ngati kuti muli pa ntchito yomwe inakupezerani makalata,kapena ngati a mpingo,olo kuti munapangidwa a doputi,olonso kuti munakwatira mereka,komanso simusunga chenje chilichonse.........ndi inuyo amene ine ndinavotelera kerry......


In short,magulu a ine ndi mbirikunjanji and others that Mukukhala ndi makalata  abwinobwino,there is little to worry about who wins.But you others,ineyo zandikhuza because Bush will be adressing makalata issues more seriously this time around.Konzekani,there are so many ways mungathandizikire.


Its sad that issues of Eminem received a huge response and yet Motherland issues dont receive that response.Samalani ndi anthu oyankhira nkhani ngati zimenezi chifukwa ndi a konko kapena akukhala pa mtendele.Lero tawonani,Bush wawinanso,just what  if.....................Musamakopeke ndi anthu amena amayankha za mwano za ku Malawi chifukwa simukudziwa kuti ali mu status yanji,anthu ena sapita ku sukulu koma makolo awo amawalipirirabe fees and hence status zawo zili bwinobe, as much as we(others) try to tell you how important it is to think of home,mumayankha kuti munabwera nokha.I hope muli ndi makalata abwino bwino,chifukwa ngati mulibe,yambani kuyangana njira.


Ngati muli ndi nkhawa ndi nkhaniyi,chonde ndilembeleni mwa chinsinsi,musandiwuze dzina lanu ndipo ndikuthandizani zoti muchite konko.


By the way ndinali nanu ku phwando la ku Atlanta,mukukhala ngati kumeneko ndi kwanu koma simuli certain.Of course mukusangalala koma ziwani kuti zinthu ziyipa posachedwapa.Ine ngati kunoko pokavota ndinamva anthu akuwinyawinya za anthu obwera kumeneko.


PEZANI MAKOBILI NDIPO KONZEKERANI KUBWERERA KUJA MUDANA NAKO(MALAWI) ,KAPENA PEZANI NJIRA YOTI MUKHALIRE MOSACHEWUKACHEWUKA AKAYAMBA KUSAKA,KAPENA TILEMBELENI NGATI MULIBE NJIRA....................................


KOMA OSATAYA MTIMA TITHANDIZANA NGATI MULI NDI CHIDWI.


OTHERWISE GULILANITHU MA LABEL OMALIDZA,GALIMOTO ZANGONGOLEZO MUNTHU WOBWERA OPANDA MAKALATA BOMA LIMALANDA.


GOOD LUCK AND MAKE WISE DECISIONS


ACHILU


JAPAN


 


 



__________________
js


Member

Status: Offline
Posts: 85
Date:
Permalink Closed

it's good to know that you care but i dought if anybody is going to seriously consider your valuable information. i could be wrong but most of us only think of now and don't really care much about "what if". they don't even have a cent to their name nor even know what school is all about. there are alot of grasshoppers out there and very few ants. to all you grasshoppers now is the time to start thinking about tomorrow we are not getting any younger. you will never have this oppoturnity again. kwanu kwanu mnthengo mudalaka njoka.


with love


jsm:



-- Edited by js at 19:39, 2004-11-03

-- Edited by js at 19:42, 2004-11-03

__________________
lyfeisgood


Veteran Member

Status: Offline
Posts: 100
Date:
Permalink Closed

Chilungamobasi, are you in Japan or USA? Just wondering how you voted in Japan.

__________________
js


Member

Status: Offline
Posts: 85
Date:
Permalink Closed

absentee ballot. you can vote from anywhere in the world.

__________________
lyfeisgood
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard