Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: MAGEMU


Veteran Member

Status: Offline
Posts: 124
Date:
MAGEMU
Permalink Closed


Some guys were overheard talking and this is what they had to say to each other.
  
Uli ndi mutu waukulu ukapita ku salon kukatsukitsa tsitsi, a hairdresser akamaliza side imodzi amatenga Taxi kuti akafike side inayo.
  
Khoma lakwanu ndilowonda maneighbours akamadula anyezi mumalira nawo.
  
Kwanu ndinu ambiri mpaka aliyense ali ndi number plate. 

Kwanu ndinu osauka mukamwa mkaka ndiye kuti ulimwana ma mumawere amayi ako
  
Inu kwanu nonse mulindi besi ndi mphaka yemwe amanena miaaw ndi besi.
  
Akuti iwe ndi iwe wamtali mpaka ukavala trouser, by the time ikufika waist yako, yatha fasho.
  
Tsitsi lako ndilolimba usanalipese ofunika umeze ma painkillers.
  
Kwanu ndinu olemera. Mpaka mphaka ndi makoswe akwanu amapita ku school.
  
Iwe ndiwe opepela. Ukamalowa mu minibus umanena odi
  
TV yakwanu ndiyaingono mpaka mumawonera ndi diso limodzi
  
Nyumba yakwanu ndiyaikulu mpaka chakudya chikachoka kukitchen, chimafika ku dining chitawola.
  
Kwanu nonse ndinu wokuda biiiiii!!! Muka lowa mu galimoto yakwanu, ma window amasanduka tinted.
  
Sistez yako ndi yaifupi, ingathe kuthamanga kunsi kwa bedi.
  
Iwe ndiwe wonenepa Ukalowa mkalasi, umakhala next to everyone.
  
Kwanu ndinu wolemera mpaka mumakazinga mazira ndi lotion.
  
Mmene umagula bubble gum koyamba, shopkeeper anakupatsira ya green. Iwe nkumati ndikufuna yakupsya
  
Tv yakwanu ndiyakale ukaiyatsa umamupeza Bakili adakali mwana
  
Kwanu ndiinu ambili koma ndinu aulesi mukakazinga dzira limodzi mumapanga photocopy.
  
Iwe ndiwe wamfupi mpaka umatsika minibus ndi parachute.
  
TV yakwanu ndiyaingono mukati muonele News, amayamba ndikunena Usiku wabwino nonse mukutiona koma?
  
TV yakwanu ndiyakale mpaka mumathimitsa ndi madzi
  
magemudi??????????????????????????????????????
  


__________________


Guru

Status: Offline
Posts: 500
Date:
Permalink Closed

Atame wrote:

Tv yakwanu ndiyakale ukaiyatsa umamupeza Bakili adakali mwana.





Ha ha!

-- Edited by awmygawd at 10:54, 2007-06-01

__________________


Guru

Status: Offline
Posts: 1277
Date:
Permalink Closed

Atame wrote:

  
Kwanu nonse ndinu wokuda biiiiii!!! Muka lowa mu galimoto yakwanu, ma window amasanduka tinted. 
  



ideablehweirdfaceconfused



__________________
If Iam not for myself,who will be for me?And if Iam only for myself,what am I?
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard