Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: UVE WABWERA KUMUDZIKUNO


Senior Member

Status: Offline
Posts: 151
Date:
UVE WABWERA KUMUDZIKUNO
Permalink Closed


PEPANI NDINASOWA KOMABE NKHANI ILI MKAMWAKAWMA KUMUDZI KUNO NDIYOTI KU NYUMBA YAMALAMULO PANOPA AKAMBILANA ZOLOLA CHIGOLO CHA AMUNA OKHAOKHA. MBUZI . AKUFUNA ANTHU AMATHANYO NGATI ZAKUNDENDE AZILOLE . KAYA KOMA AKUTI ZILI POTI A SPEAKE AKUVOMEREZA. ZIKOMO

__________________
Zikomo


Newbie

Status: Offline
Posts: 1
Date:
Permalink Closed

kodi vuto si njala,kapena mathanyula akufunawo? Ma alawansi akulandira ma MP kumakamba zopusazo shame to Nyasaland.

__________________
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us


Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard