hey guys any one out there residing in turkey cuz am there too and it will be a great thing getting to know each other; yo yo am out for the university games/ check it out
Ku Turkeyko munthuyu n'bodza. amangolota kuti Mulungu akamchengeta, ndi kumene adzapita. Munthuyo ali ku Dowa. Akugwilitsa nchito kompyuta ya kwa DC ku Boma.Amampatsa, mlonda ndalama kuti aigwilitse ntchito usiku. Inu siyani mabodzatu ati Turkey, turkey bwnaji kodi?. Funani anthu a ku Dowa, mwamva?