Poyamba zidamveka ngati njuchi za maluwa koma lero malawi wadzala ndi zambiri. Achinyamata inu mulupita nabwerera kumudzikuno muluberesa zonyasa. Ife kuno chigololochamuna okhaokha kapena atsikanaokhaokha sutuluchufuna. iayi malaulo awa.Ife malawians we dont need andwant this now no.not here please chonde.malawi isa fearing god country and we dont want that no no no. ine ndulukambaizi pomvetsedwa kuti ku mwela kwaamba bungwe lome lulufunitsisa kuti anthu amaliseche ofanafan adzithakupanga nyasi osamangidwa ndiboma. navetsedwa kuti wen ndiadziphunzitsi ndithu ndipodi alufuna akuti ma human freedom ndi democracy rights but are we people of malawi selious? am asking and answer me now. ndavetsedwa kuti pali ma mp akunyumba yamalamulo wina wakubalaka alulimkitsaizi.ku pariament nkhaniyi ulifika ndithu ndipo aluyidziwa .kaya malawiyu. ine ndulukaika ndi anthu obwera .please chonde osabweretsa nyazi kuno .kodi zowon amphunzisi wa wana wathu akhale wachambuyo kwa mwamuna mzake. ana athu ali ndi mwai wokula bwino ? akhritsu ali kuti athandize paja bingu angolola zilizonse. dama lanji kodi? zkomo anzanga titani?

Nyasa ,
Inutu mungokhala duu napenya chichitike nchani. Zinthuzi zimakhalapo chapansipansi koma zimasowa oyambitsaKodi inuyo ndekuti sinu penapake olakwa?