i agreed wif yuor views now. Are yuoa dj sir? ndidzakuyitanani pa tarven panga muzaimbe r keli yu wati. zikomo. koma bambo inu ngwopenga zedi eti . kodi inu sumuluona mavuto ena oti tingakambilanepo apa kulekana ndi njuchi la funso mulunalo. inu maganizo anu pa nyimbooyo ni chani ? sindeu yayi koma ndangokusuntha.
Nyasaland,
pepa dala,sinditha kukufotokozela za akulu amenewa chifukwa nyimbo zawo ndi za mchizungu,iwe unazolowera "kamenya choir" kapena"Lucky stars" ndiye mpovuta kuti umvetsetse,nanenso sindewu ayi koma ndankambapo.
__________________
For have I now become your enemy for telling you the truth?-Galatians 4 v16.