sichipongwe ayi,koma ground iyi ndi kwa Biwi kapena ku Chilomoni?izi ndizija makolo amakuletsa kukasewela mpira kuopa kuti uthyoka nanga ground yake imeneyi kholo lingakondwe?Palibe amene angakhulupilile kuti uku ndi ku America kwa George Bush?but are you sure this game was played in the US?Next time pliz get a better ground otherwise ife sitizamenya nawo maground ake akakhala amenewa.
One more thing,mumuuzeko referee wa chizunguyo kuti chithunzi cha ku mpira samakhala choncho,kungokhala ngati ali pansi pantengo kwa Chilinde mu std 4b(sorry I forgot that this picture was taken in Malawi)and also the guy holding the ball,yes goloboyiyo,sakhala choncho unless mukamapanga atambalale.eeeh!kapingayo tsono,ayi kumudzi kuja kuli bwino ndithu because you know what you are playing on,pakapinga kapena mu nseu osati izi.Below is another picture from a different angle:
-- Edited by Ngwazi at 05:46, 2005-06-08
__________________
For have I now become your enemy for telling you the truth?-Galatians 4 v16.
Come on people don't give these guys ahard time,this ground is in Washington DC capital of USA...it's just another country sikuti ndi kumwamba. Roca.
Roca,
kani uku ndiye ku Washington,Capital ya America?sindimadziwa kuti kuli malo ena ofanana ndi kwa Biwi ku Lilongwe,nakonso ku capital koma ya Malawi.zinthudi zimakhala ziwiri ziwiridi zoona.Now you wonder why Nyasaland akumayankhula mwano za anthu outside of Malawi,with grounds like this atinyozadi.
__________________
For have I now become your enemy for telling you the truth?-Galatians 4 v16.