Members Login
Username 
 
Password 
    Remember Me  
Post Info TOPIC: CHIBUKU POWDER

Newbie

Status: Offline
Posts: 3
Date:
CHIBUKU POWDER
Permalink Closed

This is no advert whatsoever but its just a compliment to chibuku products limited for introducing chibuku powder.I have stayed away from my daring chibuku for three yrs now.Ndakhala kuno ( UK) kwa zaka zitatu ndipo chilakolako cha chibuku(chibagi) chakhala chi kundibandula.Ndinali odabwa ndi osangalala pamene ndinalandila DHL parcel kuchokela kumalawi.Angoni azanga ananditumizila chibuku powder.Ine sindinachedwe koma kumulongosola katundu ameneyi ndipo ndanamuphika ngati thobwa ndikumumenya after two days.Ine moyo wanga pano watsika pansi popeza ndamwa mowa wathu wathuwu.This is a very good develpoment to our country and its not only good to my fellow drinkmates.Because the pack is carring malawi name on it.We may say and dream that one day we may have malawi beer in my london's the red elephant pub.we may say this one stape towards getting into exporting bussiness.BRAVO CHIBUKU.

__________________

Member

Status: Offline
Posts: 81
Date:
Permalink Closed

Hey bro,tell us in detailz how we may get this stuff here,Pliz nafenso kachibaba ka chibuku ndiye kakutipweteka.

__________________

Newbie

Status: Offline
Posts: 30
Date:
Permalink Closed

There is a party website.. check it out... in honour of the great drink itself.

www.chibuku.com

__________________
Respect is only given to those who give it without expectation of it.

Newbie

Status: Offline
Posts: 25
Date:
Permalink Closed

FoteFote wrote:

This is no advert whatsoever but its just a compliment to chibuku products limited for introducing chibuku powder.I have stayed away from my daring chibuku for three yrs now.Ndakhala kuno ( UK) kwa zaka zitatu ndipo chilakolako cha chibuku(chibagi) chakhala chi kundibandula.Ndinali odabwa ndi osangalala pamene ndinalandila DHL parcel kuchokela kumalawi.Angoni azanga ananditumizila chibuku powder.Ine sindinachedwe koma kumulongosola katundu ameneyi ndipo ndanamuphika ngati thobwa ndikumumenya after two days.Ine moyo wanga pano watsika pansi popeza ndamwa mowa wathu wathuwu.This is a very good develpoment to our country and its not only good to my fellow drinkmates.Because the pack is carring malawi name on it.We may say and dream that one day we may have malawi beer in my london's the red elephant pub.we may say this one stape towards getting into exporting bussiness.BRAVO CHIBUKU.

Man,inu musamatchubule mwina anangokutumizilani mawele oviika inu n'kumati chibuku!Kodi kwanu ndikuti?chifukwa zikuoneka ngati kumudzi simuziwako!!
Learn how to differenciate between thobwa and chibuku!!

__________________

Guru

Status: Offline
Posts: 699
Date:
Permalink Closed

Dobadoba wrote:

Powder alipo si thobwa ayi kungoti enafe sitimamwa chibuku. Ngati mukufuna powder tell me i will connect you to the main man in that business, wawa aluki zainu timadziwa mpaka list tinaona akazi opusa zitsilu mwagwa nayo.

__________________
"Gimme the weed and i will get high for i have not failed but discovered ways that just dont work"

Newbie

Status: Offline
Posts: 2
Date:
Permalink Closed

Ndikuthokoze mkulu iwe,nditawelenga ndimkagoti mbwelera,koma that day my younger brother was coming to uk and I called him ndikumufunsa anditenegele lero moti tichimwa ndikachoka ku vepi.I will send you a private message and see how can I send u one pack...Tchezi Mdala

__________________

Newbie

Status: Offline
Posts: 7
Date:
Permalink Closed

Andimva nacho mbebe ndaitanitsa changa.kaya chomwa ndekha ndi Nzungu wanga pambalipo.

__________________

Newbie

Status: Offline
Posts: 3
Date:
Permalink Closed

Mumapitilanji kunja kopanda zibagi,kuno ndiye tinakamwabe chibuku,mudzatipeza.Ambiri a kunjanu mumabeba ka two weeks kokha mukabwela kuno.hahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahahaha

__________________
Page 1 of 1  sorted by
 
Quick Reply

Please log in to post quick replies.

Tweet this page Post to Digg Post to Del.icio.us

Create your own FREE Forum
Report Abuse
Powered by ActiveBoard