This is no advert whatsoever but its just a compliment to chibuku products limited for introducing chibuku powder.I have stayed away from my daring chibuku for three yrs now.Ndakhala kuno ( UK) kwa zaka zitatu ndipo chilakolako cha chibuku(chibagi) chakhala chi kundibandula.Ndinali odabwa ndi osangalala pamene ndinalandila DHL parcel kuchokela kumalawi.Angoni azanga ananditumizila chibuku powder.Ine sindinachedwe koma kumulongosola katundu ameneyi ndipo ndanamuphika ngati thobwa ndikumumenya after two days.Ine moyo wanga pano watsika pansi popeza ndamwa mowa wathu wathuwu.This is a very good develpoment to our country and its not only good to my fellow drinkmates.Because the pack is carring malawi name on it.We may say and dream that one day we may have malawi beer in my london's the red elephant pub.we may say this one stape towards getting into exporting bussiness.BRAVO CHIBUKU.
FoteFote wrote: This is no advert whatsoever but its just a compliment to chibuku products limited for introducing chibuku powder.I have stayed away from my daring chibuku for three yrs now.Ndakhala kuno ( UK) kwa zaka zitatu ndipo chilakolako cha chibuku(chibagi) chakhala chi kundibandula.Ndinali odabwa ndi osangalala pamene ndinalandila DHL parcel kuchokela kumalawi.Angoni azanga ananditumizila chibuku powder.Ine sindinachedwe koma kumulongosola katundu ameneyi ndipo ndanamuphika ngati thobwa ndikumumenya after two days.Ine moyo wanga pano watsika pansi popeza ndamwa mowa wathu wathuwu.This is a very good develpoment to our country and its not only good to my fellow drinkmates.Because the pack is carring malawi name on it.We may say and dream that one day we may have malawi beer in my london's the red elephant pub.we may say this one stape towards getting into exporting bussiness.BRAVO CHIBUKU.
Man,inu musamatchubule mwina anangokutumizilani mawele oviika inu n'kumati chibuku!Kodi kwanu ndikuti?chifukwa zikuoneka ngati kumudzi simuziwako!! Learn how to differenciate between thobwa and chibuku!!

Powder alipo si thobwa ayi kungoti enafe sitimamwa chibuku. Ngati mukufuna powder tell me i will connect you to the main man in that business, wawa aluki zainu timadziwa mpaka list tinaona akazi opusa zitsilu mwagwa nayo.
__________________
"Gimme the weed and i will get high for i have not failed but discovered ways that just dont work"
Ndikuthokoze mkulu iwe,nditawelenga ndimkagoti mbwelera,koma that day my younger brother was coming to uk and I called him ndikumufunsa anditenegele lero moti tichimwa ndikachoka ku vepi.I will send you a private message and see how can I send u one pack...Tchezi Mdala